Revelation 17:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mafumu a pa dziko lapansi ankachita naye chigololo, ndipo anthu okhala pa dziko lapansi ankaledzera naye vinyo wa dama lakelo.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
amene mafumu a dziko anachita chigololo naye, ndipo iwo akukhala padziko analedzera ndi vinyo wa chigololo chake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mafumu a dziko lapansi amachita naye chigololo ndipo okhala pa dziko lapansi analedzera ndi vinyo wa zigololo zake.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
amene mafumu a dziko anacita cigololo naye, ndipo iwo akukhala padziko analedzera ndi vinyo wa cigololo cace.