Revelation 17:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Pano pafunika nzeru ndi kumvetsa bwino: Mitu isanu ndi iŵiri ija, ikufanizira mapiri asanu ndi aŵiri amene mkazi uja amakhalapo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pano pali mtima wakukhala nayo nzeru. Mitu isanu ndi iwiri ndiyo mapiri asanu ndi awiri amene mkazi akhalapo;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Zimenezi zikufunika kuganizira mwanzeru. Mitu isanu ndi iwiriyo ndi mapiri asanu ndi awiri pomwe mkazi uja amakhalirapo. Yomweyonso ndi mafumu asanu ndi awiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pano pali mtima wakukhaia nayo nzeru. Mitu isanu ndi iwiri ndiyo mapiri asanu ndi awiri amene mkazi akhalapo;