Revelation 18:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwo adzaima patali chifukwa cha kuwopsedwa ndi mazunzo ake. Ndipo adzanena kuti, “Uli ndi tsoka, uli ndi tsoka, iwe Babiloni, mzinda wotchuka, mzinda wamphamvu! Pa ora limodzi lokha chilango chako chakugwera.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
chifukwa chakuopa chizunzo chake, nanena, Tsoka, tsoka, mudzi waukuluwo, Babiloni, mudzi wolimba! Pakuti m'ora limodzi chafika chiweruziro chanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo adzayima kutali nalira chifukwa choopsedwa ndi mazunzo ake. “ ‘Tsoka! Tsoka mzinda waukulu iwe, Babuloni mzinda wamphamvu! Mu ora limodzi chiwonongeko chako chafika!’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
cifukwa cakuopa cizunzo cace, nanena, Tsoka, tsoka, mudzi waukuruwo, Babulo, mudzi wolimba! pakuti m'ora limodzi cafika ciweruziro canu.