Revelation 18:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu ogulitsa zimenezi, amene adalemerera pa iye, adzaima patali chifukwa cha kuwopsedwa ndi mazunzo ake. Adzalira ndi kumva chisoni kwambiri,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Otsatsa izi, olemezedwa nao, adzaima patali chifukwa cha kuopa chizunzo chake, nadzalira, ndi kuchita chifundo;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amalonda amene anagulitsa zinthu izi napeza chuma kuchokera kwa iye adzayima patali potero ataopsedwa ndi mazunzo ake. Adzalira ndi kukhuza maliro
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Otsatsa izi, olemezedwa nao, adzaima patali cifukwa ca kuopa cizunzo cace, nadzalira, ndi kucita cifundo;