Revelation 18:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma pa ora limodzi lokha chuma chonsechi chaonongeka.” Onse oyendetsa zombo, onse oyenda pa nyanja, antchito apazombo, ndi onse oyendetsa malonda ao pa nyanja, adaima patali.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti m'ora limodzi chasanduka bwinja chuma chachikulu chotere. Ndipo watsigiro aliyense, ndi yense wakupita panyanja pakutipakuti, ndi amalinyero, ndi onse amene amachita kunyanja, anaima patali,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chuma chambiri choterechi chafika powonongeka mu ora limodzi!’ “Oyendetsa sitima ndi onse oyenda pa sitima ya pamadzi, ogwira ntchito mʼsitima ndi onse amene amadalira nyanja pamoyo wa tsiku ndi tsiku adzayima patali potero.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti m'ora limodzi casanduka bwinja cuma cacikuru cotere. Ndipo watsigiro ali yense, ndi yense wakupita panyanja pakuti pakuti, ndi amarinyero, ndi onse amene amacita kunyanja, anaima patali,