Revelation 18:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pambuyo pake mngelo wina wamphamvu adanyamula mwala, kukula kwake ngati chimphero. Adauponya m'nyanja nanena kuti, “Umu ndi m'mene Babiloni, mzinda wotchuka uja, “Udzaponyedwere pansi mwamphamvu, ndipo sudzapezekanso.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mngelo wolimba ananyamula mwala ngati mphero yaikulu, naiponya m'nyanja, nanena, Chotero Babiloni, mudzi waukulu, udzapasulidwa kolimba, ndipo sudzapezedwanso konse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka mngelo wamphamvu ananyamula mwala waukulu ngati mphero yayikulu nawuponya mʼnyanja nanena kuti, “Mwa mphamvu chonchi mzinda waukulu wa Babuloni udzaponyedwa pansi, sudzapezekanso.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mngelo wolimba ananyamula mwala, ngati mphero yaikuru, naiponya m'nyanja, nanena, Cotero Babulo, mudzi waukuru, udzapasulidwa kolimba, ndipo sudzapezedwanso konse.