Revelation 18:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja machimo ake ndi ofika mpaka ku thambo, ndipo Mulungu wakhala akukumbukira ntchito zake zoipa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pakuti machimo ake anaunjikizana kufikira m'Mwamba, ndipo Mulungu anakumbuka zosalungama zake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
pakuti machimo ake awunjikana mpaka kumwamba, ndipo Mulungu wakumbukira milandu yake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
pakuti macimo ace anaunjikizana kufikira m'Mwamba, ndipo Mulungu anakumbuka zosalungama zace.