Revelation 19:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ena onse adaphedwa ndi lupanga lija lotuluka m'kamwa mwa wokwera pa kavalo uja. Ndipo mbalame zonse zidadya ndi kukhuta mnofu wa anthuwo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo otsalawa anaphedwa ndi lupanga la Iye wakukwera pa kavalo, ndilo lotuluka m'kamwa mwake; ndipo mbalame zonse zinakhuta ndi nyama zao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ena onse anaphedwa ndi lupanga lija linatuluka mʼkamwa mwa wokwera pa kavalo uja, ndipo mbalame zonse zinadya mokwanira mnofu wa anthu akufawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo otsalawa anaphedwa ndi lupanga la iye wakukwera pa kavalo, ndilo lo turuka m'kamwa mwace; ndipo mbalame zonse zinakhuta ndi nyama zao.