Revelation 19:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kachiŵiri mau aja adanenanso kuti, “Aleluya! Utsi wa mzindawo udzakwera kumwamba mpaka muyaya.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anatinso, Aleluya. Ndipo utsi wake ukwera kunthawi za nthawi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo anafuwulanso kuti, “Haleluya! Utsi wochokera kwa mkazi wadamayo udzakwera kumwamba mpaka muyaya.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anatinso, Aleluya. Ndipo utsi wace ukwera ku nthawi za nthawi.