Revelation 19:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo mngelo uja adandiwuza kuti, “Lemba mau aŵa akuti, ‘Ngodala anthu oitanidwa ku phwando la ukwati wa Mwanawankhosa uja’.” Adandiwuzanso kuti, “Mau ameneŵa ndi mau oona a Mulungu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ananena ndi ine, Lemba, Odala iwo amene aitanidwa kuphwando la ukwati wa Mwanawankhosa. Ndipo ananena ndi ine, Iwo ndiwo mau oona a Mulungu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka mngelo anandiwuza kuti, “Lemba kuti, Odala amene ayitanidwa ku phwando la ukwati wa Mwana Wankhosa.” Ndipo anatinso, “Awa ndiwo mawu woona a Mulungu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ananena ndi ine, Lemba, Odala iwo amene aitanidwa ku phwando la ukwati wa Mwanawankhosa. Ndipo ananena ndi ine, Iwo ndiwo mau oona a Mulungu.