Revelation 2:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Mtsogoleri wa mpingo wa ku Pergamo umlembere kuti: Naŵa mau ochokera kwa uja ali ndi lupanga lakuthwa konsekonse lija.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kwa mngelo wa Mpingo wa ku Pergamo lemba: Izi anena Iye wokhala nalo lupanga lakuthwa konsekonse:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Lembera mngelo wa mpingo wa ku Pergamo kuti: Awa ndi mawu ochokera kwa amene ali ndi lupanga lakuthwa konsekonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kwa mngelo wa Mpingo wa ku Pergamo lemba: Izi anena iye wokhala nalo lupanga lakuthwa konse konse: