Revelation 2:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mutembenuke mtima tsono. Mukapanda kutero, ndidzabwera kwanuko posachedwa, ndipo ndidzakuthirani nkhondo ndi lupanga lotulukira m'kamwa mwanga lija.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake lapa; ukapanda kutero ndidza kwa iwe posachedwa, ndipo ndidzachita nao nkhondo ndi lupanga la m'kamwa mwanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono tembenukani mtima. Mukapanda kutero, ndidzabwera kwanuko posachedwa ndipo ndidzachita nanu nkhondo ndi lupanga lotuluka mʼkamwa mwanga lija.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace lapa; ukapanda kutero ndidza kwa iwe posacedwa, ndipo ndidzacita nao nkhondo ndi lupanga la m'kamwa mwanga.