Revelation 2:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akuti: Ntchito zanu zonse ndikuzidziŵa. Ndikudziŵa chikondi chanu, kukhulupirika kwanu, kutumikira kwanu, ndi kupirira kwanu kosatepatepa. Ndikudziŵa kuti ntchito zanu zatsopano nzabwino koposa zoyamba zija.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndidziwa ntchito zako, ndi chikondi, ndi chikhulupiriro, ndi utumiki, ndi chipiriro chako, ndi kuti ntchito zako zotsiriza zichuluka koposa zoyambazo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye akuti: Ndimadziwa ntchito zanu, chikondi chanu ndi chikhulupiriro chanu, kutumikira kwanu ndi kupirira kwanu. Ndikudziwa tsopano kuti ntchito zanu ndi zabwino kuposa zoyamba zija.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
1 Ndidziwa nchito zako, ndi cikondi, ndi cikhulupiriro, ndi utumiki, ndi cipiriro cako, ndi kuti nchito zako zotsiriza cicuruka koposa zoyambazo.