Revelation 2:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidampatsa nthaŵi kuti atembenuke mtima, koma safuna kutembenuka ndi kuleka kusakhulupirika kwake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndampatsa iye nthawi kuti alape; koma safuna kulapa kusiyana nacho chigololo chake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndamupatsa nthawi kuti aleke zachigololo zake koma sakufuna.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndanpatsa iye nthawi kuti alape; koma safuna kulapa kusiyana naco cigololo cace.