Revelation 2:27 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adzailamulira ndi ndodo yachitsulo, nadzaiphwanyaphwanya ngati mbiya. Ulamuliro umenewu ndi womwe Ine ndidaulandira kwa Atate.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo adzawalamulira ndi ndodo yachitsulo, monga zotengera za woumba mbiya ziphwanyika mapale; monga Inenso ndalandira kwa Atate wanga;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Adzayilamulira ndi ndodo yachitsulo ndipo nadzayiphwanyaphwanya ngati mbiya. Ulamuliro umenewu ndi omwe ndinalandira kwa Atate anga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo 7 adzawalamulira ndi ndodo yacitsulo, monga zotengera za woumba mbiya ziphwanyika mapale; monga lnenso ndalandira kwa Atate wanga;