Revelation 2:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndinudi opirira kolimba, ndipo mwasauka kwambiri chifukwa cha Ine, osatopa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo uli nacho chipiriro, ndipo walola chifukwa cha dzina langa, wosalema.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwe wapirira ndipo wakumana ndi zovuta chifukwa cha dzina langa, ndipo sunatope.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo uli naco cipiriro, ndipo walola cifukwa ca dzina langa, wosalema.