Revelation 2:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komabe chokomera chanu ndi ichi chakuti, mumadana ndi zochita za Anikolai, zimene inenso ndimadana nazo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ichi uli nacho, kuti udana nazo ntchito za Anikolai, zimene Inenso ndidana nazo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Komabe chokomera chako ndi chakuti umadana ndi zochita za Anikolai, zimene Inenso ndimadana nazo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ici uli naco, kuti udana nazo nchito za Anikalai, zimene Inenso ndidana nazo.