Revelation 21:25 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zitseko za pa zipata zake zidzakhala zosatseka tsiku lonse, chifukwa kumeneko kudzakhala kulibe usiku.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pazipata zake sipatsekedwa konse usana, (pakuti sikudzakhala usiku komweko);
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zipata zake sizidzatsekedwa ngakhale tsiku limodzi lomwe pakuti sikudzakhala usiku kumeneko.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo 3 pa zipata zace sipatsekedwa konse usana, 4 (pakuti sikudzakhala usiku komweko);