Revelation 21:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Aliyense amene adzapambane, adzalandira zimenezi, ndipo Ine ndidzakhala Mulungu wake, iye adzakhala mwana wanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iye wakupambana adzalandira izi; ndipo ndidzakhala Mulungu wake, ndi iye adzakhala mwana wanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye amene adzapambane adzalandira zonsezi, ndipo ndidzakhala Mulungu wake ndi Iye adzakhala mwana wanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iye wakulakika adzalandira izi; ndipo ndidzakhala Mulungu wace, ndi iye adzakhala mwana wanga.