Revelation 22:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adandiwuzanso kuti, “Usabise mau a m'buku lino oneneratu zam'tsogolo, pakuti nthaŵi yake ili pafupi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ananena ndi ine, Usasindikiza chizindikiro mau a chinenero cha buku ili; pakuti nthawi yayandikira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka anandiwuza kuti, “Usabise mawu onena zamʼtsogolo a mʼbuku ili chifukwa nthawi yayandikira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ananena ndi ine, Usasindikiza cizindikilo mau a cinenero ca buku ili; pakuti nthawi yayandikira.