Revelation 3:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndikubwera posachedwa. Gwiritsani chimene muli nacho, kuti wina angakulandeni mphotho yanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndidza msanga; gwira chimene uli nacho, kuti wina angalande korona wako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndikubwera msanga. Gwiritsitsa chimene uli nacho kuti wina angakulande chipewa chako chaufumu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndidza msanga; gwira cimene uli naco, kuti wina angalande korona wako.