Revelation 3:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma popeza kuti ndinu ofunda chabe, osati otentha kapena ozizira, ndidzakusanzani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kotero, popeza uli wofunda, wosati wotentha kapena wozizira, ndidzakulavula m'kamwa mwanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono popeza ndiwe wofunda chabe, sindiwe wotentha kapena wozizira, ndatsala pangʼono kuti ndikulavule mʼkamwa mwanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kotero, popeza uti wofunda, wosati wotentha kapena wozizira, ndidzakulabvula m'kamwa mwanga.