Revelation 3:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Dzukani, ndi kulimbitsa zokutsalirani zimene zili pafupi kutha. Pakuti ndikuwona kuti ntchito zanu sizili zangwiro konse pamaso pa Mulungu wanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Khala wodikira, ndipo limbitsa zotsalira zimene zinafuna kufa; pakuti sindinapeza ntchito zako zakufikira pamaso pa Mulungu wanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Dzuka! Limbitsa zimene zatsalira zomwe zatsala pangʼono kufa, pakuti ndaona kuti ntchito zako nʼzosakwanira pamaso pa Mulungu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Khala wodikira, ndipo limbitsa zotsalira, zimene zinafuna kufa; pakutisindinapeza nchito zako zakufikira pamaso pa Mulungu wanga.