Revelation 3:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma alipo angapo pakati panu ku Sardi amene sadadetse zovala zao. Iwowo adzayenda nane pamodzi atavala zoyera, pakuti ndi oyeneradi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Komatu uli nao maina owerengeka m'Sardi, amene sanadetsa zovala zao; ndipo adzayenda ndi Ine m'zoyera; chifukwa ali oyenera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Komabe uli ndi anthu angapo mu Sarde amene sanadetse zovala zawo. Amenewa adzayenda ndi Ine atavala zoyera popeza ndi oyenera kutero.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Komatu uli nao maina owerengeka m'Sarde, amene sanadetsa zobvala zao; ndipo adzayenda ndi Ine m'zoyera; cifukwa ali oyenera.