Revelation 5:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kenaka ndidaona mngelo wamphamvu akufunsa mokweza mau kuti, “Ndani ali woyenera kufutukula bukuli ndi kumatula zimatiro zake?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndinaona mngelo wamphamvu wakulalikira ndi mau akulu, Ayenera ndani kutsegula buku, ndi kumasula zizindikiro zake?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo ndinaona mngelo wamphamvu akulengeza ndi mawu okweza kuti, “Ndani ali woyenera kumatula zomatira ndi kufutukula bukuli?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndinaona mngelo wamphamvu wakulalikira ndi mau akuru, Ayenera ndani kutsegula buku, ndi kumasula zizindikilo zace?