Revelation 5:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma panalibe ndi mmodzi yemwe Kumwamba, kapena pa dziko lapansi, kapena kunsi kwa dziko, wotha kufutukula bukulo kapena kuyang'anamo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo sanathe mmodzi m'Mwamba, kapena padziko, kapena pansi pa dziko kutsegula pabukupo, kapena kulipenya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma panalibe ndi mmodzi yemwe kumwamba kapena pa dziko lapansi kapena kunsi kwa dziko lapansi woti afutukule bukulo kapena kuona zamʼkati mwake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo sanathe mmodzi m'Mwamba, kapena padziko, kapena pansi pa dziko kutsegula pabukupo, kapena kulipenya.