Revelation 5:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero ndidalira kwambiri poona kuti sadapezeke woyenera kufutukula bukulo kapena kuyang'anamo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndinalira kwambiri, chifukwa sanapezedwa mmodzi woyenera kutsegula bukulo, kapena kulipenya;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndinalira kwambiri chifukwa panalibe amene anapezeka woyenera kufutukula bukuli kapena kuona zamʼkati mwake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndinalira kwambiri, cifukwa sanapezedwa mmodzi woyenera kutsegula bukulo, kapena kulipenya;