Revelation 5:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iyeyo adabwera nkulandira buku lija limene linali m'dzanja lamanja la wokhala pampando wachifumu uja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anadza, nalitenga kudzanja lamanja la Iye wakukhala pa mpando wachifumu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anabwera natenga buku lija limene linali mʼdzanja lamanja la wokhala pa mpando waufumuyo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anadza, nalitenga ku dzanja lamanja la Iye wakukhala pa mpando wacifumu.