Revelation 6:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kenaka Mwanawankhosa uja adamatula chimatiro chachiŵiri. Ndipo ndidamva Chamoyo chachiŵiri chija chikunena kuti, “Bwera!”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pamene anamasula chizindikiro chachiwiri, ndinamva chamoyo chachiwiri nichinena, Idza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwana Wankhosa atatsekula chomatira chachiwiri, ndinamva chamoyo chachiwiri chija chikuti, “Bwera!”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pamene anamasula cizindikilo caciwiri, ndinamva camoyo caciwiri nicinena, Idza.