Revelation 6:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kenaka Mwanawankhosa uja adamatula chimatiro chachinai. Ndipo ndidamva Chamoyo chachinai chija chikunena kuti, “Bwera!”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pamene anamasula chizindikiro chachinai, ndinamva mau a chamoyo chachinai nichinena, Idza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwana Wankhosa atatsekula chomatira chachinayi, ndinamva chamoyo chachinayi chija chikunena kuti, “Bwera!”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pamene anamasula cizindikilo cacinai, ndinamva mau a camoyo cacinai nicinena, Idza.