Revelation 7:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo mmodzi mwa Akuluakulu aja adandifunsa kuti, “Kodi ovala mikanjo yoyeraŵa ndani, ndipo achokera kuti?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mmodzi wa akulu anayankha, nanena ndi ine, Iwo ovala zovala zoyera ndiwo ayani, ndipo achokera kuti?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamenepo mmodzi wa akuluakulu aja anandifunsa kuti, “Kodi avala mikanjo yoyerawa ndani ndipo akuchokera kuti?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mmodzi wa akuru anayankha, nanena ndi ine, Iwo obvala zobvala zoyera ndiwo ayani, ndipo acokera kuti?