Revelation 7:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwo sadzamvanso njala kapena ludzu. Sadzaombedwanso ndi dzuŵa kapena kusauka ndi kutentha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
sadzamvanso njala, kapena ludzu, kapena silidzawatentha dzuwa, kapena chitungu chilichonse;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
‘Iwowa sadzamvanso njala, sadzamvanso ludzu, dzuwa kapena kutentha kulikonse sikudzawawotcha.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
sadzamvanso njala, kapena ludzu, kapena, silidzawatentha dzuwa, kapena citungu ciri conse;