Revelation 7:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adaŵauza kuti, “Musaononge msanga dziko, kapena nyanja, kapenanso mitengo, tiyambe taŵalemba chizindikiro pa mphumi atumiki a Mulungu wathu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nanena, Musaipse dziko, kapena nyanja, kapena mitengo, kufikira tidasindikiza chizindikiro akapolo a Mulungu wathu, pamphumi pao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Musawononge dziko, nyanja ndi mitengo kufikira titalemba chizindikiro pa mphumi za atumiki a Mulungu wathu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nanena, Musaipse dziko, kapena nyanja, kapena mitengo, kufikira tidasindikiza cizindikilo akapolo a Mulungu wathu, pamphumi pao.