Revelation 9:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthuwo sadatembenukenso kuti aleke kupha anzao, ufiti, dama ndi kuba.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo sanalapa mbanda zao, kapena nyanga zao, kapena chigololo chao, kapena umbala wao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Sanalapenso kuleka zakupha, zamatsenga awo, zachigololo zawo kapena umbava wawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo sanalapa mbanda zao, kapena nyanga zao, kapena cigololo cao, kapena umbala wao.