Revelation 9:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Silidaloledwe kuŵapha, koma kungoŵazunza pa miyezi isanu. Kuŵaŵa kwake kwa mazunzowo kunkalingana ndi ululu wa chinkhanira chikaluma munthu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anapatsa ilo mphamvu si kuti likawaphe, komatu kuti likawazunze miyezi isanu; ndipo mazunzidwe ao anali ngati mazunzidwe a chinkhanira, pamene chiluma munthu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Silinapatsidwe mphamvu yowapha koma yowazunza kwa miyezi isanu. Ndipo ululu umene anthuwo anawumva unali ngati wa chinkhanira chikaluma munthu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anapatsa ilo mphamvu si kuti likawaphe, komatu kuti likawazunze miyezi isanu; ndipo mazunzidwe ao anali ngati mazunzidwe a cinkhanira, pamene ciluma munthu.