Romans 1:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndimampempha Mulunguyo kuti ndipeze mpata tsopano woti ndibwere kwanuko.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi kupempha masiku onse m'mapemphero anga, ngati nkutheka tsopano mwa chifuniro cha Mulungu, ndione ulendo wabwino, wakudza kwa inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mʼmapemphero anga, nthawi zonse, ndimapemphera kuti ngati nʼkotheka mwachifuniro cha Mulungu, njira inditsekukire kuti ndibwere kwanuko.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ngati nkutheka tsopano mwa cifuniro ca Mulungu, ndione ulendo wabwino, wakudza kwa inu.