Romans 1:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Makamaka ndinene kuti tikalimbikitsane pamene ndidzakhale pakati panu. Inu mudzandilimbikitsa ndi chikhulupiriro chanu, ine nkukulimbikitsani ndi chikhulupiriro changa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndiko, kuti ine ndikatonthozedwe pamodzi ndi inu, mwa chikhulupiriro cha ife tonse awiri, chanu ndi changa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndiponso kuti tonsefe tilimbikitsane mʼchikhulupiriro wina ndi mnzake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndiko, kuti ine ndikatonthozedwe pamodzi ndi inu, mwa cikhulupiriro ca ife tonse awiri, canu ndi canga.