Romans 1:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndili ndi udindo wolalikira anthu ovumbuluka ndi osavumbuluka, ndiwo anzeru ndi opulukira omwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ine ndili wamangawa wa Agriki ndi wa akunja, wa anzeru ndi wa opusa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndi wokakamizidwa ndi udindo wotumikira Agriki pamodzi ndi omwe si Agriki, kwa anzeru ndi kwa opusa omwe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ine ndiri wamangawa wa Ahelene ndi wa akunja, wa anzeru ndi wa opusa.