Romans 1:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chimenechi ndicho chikundikakamiza kukalalika Uthenga Wabwino kwa inunso a ku Roma.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chotero, momwe ndingakhoze ine, ndilikufuna kulalikira Uthenga Wabwino kwa inunso a ku Roma.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa chifukwa chimenechi, ine ndikufunitsitsa kulalikira Uthenga Wabwino kwa inunso amene muli ku Roma.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cotero, momwe ndingakhoze ine, ndirikufuna kulalikira Uthenga Wabwino kwa inunso a ku Roma.