Romans 1:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Umasimba za Mwana wake, Yesu Ambuye athu. Poyang'anira umunthu wake, kholo lake ndi Davide,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
wakunena za Mwana wake, amene anabadwa, wa mbeu ya Davide, monga mwa thupi,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Uthengawu ndi wonena za Mwana wake amene mwa umunthu wake anali wochokera mwa Davide.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
wakunena za Mwana wace, amene anabadwa, wa mbeu ya Davide, monga mwa thupi,