Romans 10:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndi monga momwe mau a Mulungu anenera kuti, “Aliyense amene adzatama dzina la Ambuye mopemba adzapulumuka.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pakuti, amene aliyense adzaitana pa dzina la Ambuye adzapulumuka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
pakuti, “Aliyense amene adzayitana pa dzina la Ambuye adzapulumuka.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
pakuti, amene ali yense adzaitana pa dzina la Ambuye adzapulumuka.