Romans 10:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma si onse amene adalandira Uthenga Wabwinowo. Ndi monga mneneri Yesaya anenera kuti, “Ambuye, ndani adakhulupirira zimene tidalalika?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma sanamvera Uthenga Wabwino onsewo. Pakuti Yesaya anena, Ambuye, anakhulupirira ndani zonena ife?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma si onse amene anavomereza Uthenga Wabwino. Pakuti Yesaya akuti, “Ambuye, ndani amene wakhulupirira uthenga wathu?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma sanamvera Uthenga Wabwino onsewo. Pakuti Yesaya anena, Ambuye, anakhulupirira ndani zonena ife?