Romans 10:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndikuŵachitira umboni kuti ndi achangudi pa zinthu za Mulungu, koma changu chake sadachimvetse bwino m'mene chiyenera kukhalira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti ndiwachitira iwo umboni kuti ali ndi changu cha kwa Mulungu, koma si monga mwa chidziwitso.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Popeza ndiwachitira umboni kuti ndi achangu pa zinthu za Mulungu koma osati mwachidziwitso.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti ndiwacitira iwo umboni kuti a ali ndi cangu ca kwa Mulungu, koma si monga mwa cidziwitso.