Romans 10:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo Yesaya adaanena molimba mtima kuti, “Adandipeza anthu amene sanali kundifunafuna. Ndidaŵaonekera anthu amene sankafunsa za Ine.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yesaya alimbika mtima ndithu, nati, Ndinapezedwa ndi iwo amene sanandifuna; ndinaonekera kwa iwo amene sanandifunsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Yesaya molimba mtima akuti, “Anandipeza anthu amene sanali kundifunafuna. Ndinadzionetsera kwa amene sanafunse za Ine.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yesaya alimbika mtima ndithu, nati, Ndinapezedwa ndi iwo amene sanandifuna; Ndinaonekera kwa iwo amene sanandifunsa.