Romans 10:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma za Aisraele adati, “Tsiku lonse ndidatambalitsa manja anga kwa mtundu wa anthu osandimvera ndi ondiwukira Ine.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma kwa Israele anena, Dzuwa lonse ndinatambalitsira manja anga kwa anthu osamvera ndi okanakana.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma zokhudzana ndi Aisraeli akuti, “Tsiku lonse ndinatambasulira manja anga kwa anthu osandimvera ndi okanika.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma kwa Israyeli anena, Dzuwa lonse ndinatambalitsira manja anga kwa anthu osamvera ndi okanakana.