Romans 10:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma kunena za chilungamo chimene chimapezeka pakukhulupirira, akuti, “Mumtima mwako usanene kuti, ‘Ndani adzakwera Kumwamba?’ ” (Ndiye kuti kukamuuza Khristu kuti atitsikire ife.)
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma chilungamo cha chikhulupiriro chitero, Usamanena mumtima mwako, Adzakwera ndani Kumwambako? Ndiko, kutsitsako Khristu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma chilungamo cha chikhulupiriro chikuti, “Usanene mu mtima mwako kuti, ‘Kodi ndani amene akwere kumwamba?’ ” (ndiko, kukatsitsa Khristu)
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma cilungamo ca cikhulupiriro citero, Usamanena mumtima mwako, Adzakwera ndani Kumwambako? ndiko, kutsitsako Kristu;