Romans 10:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Usanenenso kuti, ‘Ndani adzatsikira ku dziko la anthu akufa?’ ” (Ndiye kuti kukamubwezera Khristu kuchokera ku dziko la anthu akufa.)
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kapena, Adzatsikira ndani ku chiphompho chakuya? Ndiko, kukweza Khristu kwa akufa,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“kapena ‘Ndani adzatsikira ku dziko la anthu akufa?’ ” (ndiko, kukamutenga Khristu kwa akufa).
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kapena, Adzatsikira ndani kudzenieko? ndiko, kukweza Kristu kwa akufa.