Romans 11:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Maso ao atsekedwe kuti asapenye, ndipo msana wao ukhale wopindika nthaŵi zonse.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
maso ao adetsedwe, kuti asapenye, ndipo muweramitse msana wao masiku onse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Maso awo atsekedwe kuti asaone, ndi misana yawo ikhale yokhota nthawi zonse.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Maso ao adetsedwe, kuti asapenye, Ndipo muweramitse msana wao masiku onse.