Romans 11:26 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo Aisraele onse adzapulumuka. Ndi monga Malembo anenera kuti, “Mpulumutsi adzachokera ku Ziyoni, adzachotsera zidzukulu za Yakobe kuipa kwao konse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo chotero Israele yense adzapulumuka; monganso kunalembedwa, kuti, Adzatuluka ku Ziyoni Mpulumutsi; Iye adzachotsa zamwano kwa Yakobo:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kotero tsono Aisraeli onse adzapulumuka, monga kwalembedwa kuti, “Mpulumutsi adzachokera ku Ziyoni; Iye adzachotsa zoyipa zonse za Yakobo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo cotero Israyeli yense adzapulumuka; monganso kunalembedwa, kuti, Adzaturuka ku Ziyoni Mpulumutsi; Iye adzacotsa zamwano kwa Yakobo: