Romans 11:30 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kale inu a mitundu ina simunkamvera Mulungu, koma tsopano Mulungu akukuchitirani chifundo chifukwa cha kusamvera kwa Ayuda.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti monga inunso kale simunamvera Mulungu, koma tsopano mwalandira chifundo mwa kusamvera kwao,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Monga mmene inu munalili, osamvera Mulungu pa nthawi ina, tsopano mwalandira chifundo chifukwa cha kusamvera kwawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti 2 monga inunso kale simunamvera Mulungu, koma tsopano mwalandira cifundo mwa kusamvera kwao,